DOWNLOAD NTHAWI - MP3, MP4 & LYRICS

Title Nthawi
Artists
Genres Afropop
Country Malawi

Nthawi Lyrics

M'dalitso wako udzatsika 
Chisomo chake chidzatsika 
Nthawi yako idzafika 
Nyengo zako zidzasintha

Chilichonse chomwe udzagwire 
Chidzabala zipatso, chidzabala zipatso 
Thembelero lawo lidzakhala m'dalitso 
Manyozo adzakhala matamando 
Madando ako adzapeza mayankho

Nthawi, Nthawi idzafika 
Nthawi idzafika, nthawi idzafika 
Chimwemwe sindalama ai 
Usauzunze mtima 
Nthawi idzafika

Nthawi, Nthawi idzafika 
Nthawi idzafika, nthawi idzafika 
Chimwemwe sindalama ai 
Usauzunze mtima 
Nthawi idzafika

Kupambana kosatha 
Mtendere uzadza 
Mavuto adzatha, ingokhulupilira 
Sudzasowa kanthu 
Sudzanyozekanso 
Sudzaderanso nkhawa

Chilichonse olo usanapemphe 
Ambuye adzapatsa, Ambuye adzapatsa 
Thembelero lawo lidzakhala m'dalitso
Manyozo adzakhala matamando
Madando ako adzapeza mayankho
Oh, oh

Nthawi, Nthawi idzafika
Nthawi idzafika, Nthawi idzafika
Chimwemwe sindalama ai
Usauzunze mtima
Nthawi idzafika

Nthawi, Nthawi idzafika
Nthawi idzafika, Nthawi idzafika
Chimwemwe sindalama ai
Usauzunze mtima
Nthawi idzafika

Zonse umakhumba, umafuna 
Osakakamiza... 
Nthawi, Nthawi nthawi